Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 35:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi akulu ace anapatsa nsembe yaufulu kwa anthu, kwa ansembe, ndi kwa Alevi. Hilikiya ndi Zekariya ndi Yehieli, atsogoleri a m'nyumba ya Mulungu, anapatsa ansembe zoweta zazing'ono zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi limodzi, ndi ng'ombe mazana atatu, zikhale nsembe za Paskha.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35

Onani 2 Mbiri 35:8 nkhani