Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 35:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anyamata ace anamturutsa m'gareta, namuika m'gareta waciwiri anali naye, nabwerera naye ku Yerusalemu; nafa iye naikidwa m'manda a makolo ace. Ayuda onse ndi Yerusalemu nalira Yosiya.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35

Onani 2 Mbiri 35:24 nkhani