Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 35:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi oyimbira, ana a Asafu, anali pokhala pao, monga adalamulira Davide, ndi Asafu, ndi Hemani, ndi Yedutuni mlauli wa mfumu; ndi olindirira anali pa zipata zonse, analibe kuleka utumiki wao; pakuti abale ao Alevi anawakonzera

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35

Onani 2 Mbiri 35:15 nkhani