Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 34:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yosiya nacotsa zonyansa zonse m'maiko onse okhala a ana a Israyeli, natumikiritsa onse opezeka m'lsrayeli, inde kutumikira Yehova Mulungu wao. Masiku ace onse iwo sanapambuka kusamtsata Yehova Mulungu wa makolo ao.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 34

Onani 2 Mbiri 34:33 nkhani