Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 34:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inaimirira pokhala pace, nicita pangano pamaso pa Yehova, kuti adzayenda cotsata Yehova, ndi kusunga malamulo ace, ndi mboni zace, ndi malemba ace, ndi mtima wace wonse, ndi moyo wace wonse, kucita mau a cipangano olembedwa m'bukumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 34

Onani 2 Mbiri 34:31 nkhani