Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 33:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anamanganso misanje adaipasula Hezekiya atate wace, nautsira Abaala maguwa a nsembe, napanga zifanizo, nalambira khamu lonse la kuthambo, nalitumikira.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 33

Onani 2 Mbiri 33:3 nkhani