Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 33:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Citatha ici tsono iye anaumangira mudzi wa Davide linga lakunja, kumadzulo kwa Gihoni, m'cigwa, mpaka polowera pa cipata cansomba; nazinga Ofeli, nalikweza kwambiri; anaikanso akazembe a nkhondo m'midzi yonse yamalinga ya m'Yuda.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 33

Onani 2 Mbiri 33:14 nkhani