Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 32:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamodzi ndi iye pali dzanja la thupi lanyama; koma pamodzi ndi ife pali Yehova Mulungu wathu, kutithandiza ndi kutigwirira nkhondo. Ndipo anthu anacirikizika ndi mau a Hezekiya mfumu ya Yuda.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 32

Onani 2 Mbiri 32:8 nkhani