Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 31:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naikanso gawo la mfumu lotapa pa cuma cace la nsembe zopsereza, ndilo la nsembe zopsereza za m'mawa ndi madzulo, ndi la nsembe zopsereza za masabata, ndi za pokhala mwezi, ndi za nyengo zoikika, monga mulembedwa m'cilamulo ca Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 31

Onani 2 Mbiri 31:3 nkhani