Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 30:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono amtokoma anamuka ndi akalata ofuma kwa mfumu ndi akuru ace mwa Israyeli ndi Yuda lonse, monga inauza mfumu ndi kuti, Inu ana a Israyeli, bwerani kwa Yehova Mulungu wa Abrahamu, Isake, ndi Israyeli, kuti Iye abwere kwa otsala anu opulumuka m'dzanja la mafumu a Asuri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 30

Onani 2 Mbiri 30:6 nkhani