Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 30:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Hezekiya mfumu ya Yuda anapatsa msonkhano ng'ombe cikwi cimodzi, ndi nkhosa zikwi zisanu ndi ziwiri; ndi akuru anapatsa msonkhano ng'ombe cikwi cimodzi, ndi nkhosa zikwi khumi; ndipo ansembeambiri adadzipatula,

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 30

Onani 2 Mbiri 30:24 nkhani