Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 30:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hezekiya ananena motonthoza mtima kwa Alevi onse akuzindikira bwino za utumiki wa Yehova. Ndipo anadya pamkomano masiku asanu ndi awiri, naphera nsembe zoyamika, ndi kulemekeza Yehova Mulungu wa makolo ao.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 30

Onani 2 Mbiri 30:22 nkhani