Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamanga malo opatulikitsa, m'litali mwace monga mwa kupingasa kwa nyumba mikono makumi awiri, ndi kupingasa kwace mikono makumi awiri; naikuta ndi golidi wabwino wakufikira matalente mazana asanu ndi limodzi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 3

Onani 2 Mbiri 3:8 nkhani