Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 29:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipoanabweranazong'ombe zisanundi ziwiri, ndi nkhosa zamphongo zisanu ndi ziwiri ndi ana a nkhosa asanu ndi awiri, ndi atonde asanu ndi awiri, zikhale nsembe yaucimo ya ufumu, ndi ya malo opatulika, ndi ya Yuda. Ndipo anawauza ansembe ana a Aroni azipereke pa guwa la nsembe la Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 29

Onani 2 Mbiri 29:21 nkhani