Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 29:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo analowa m'katimo kwa mfumu Hezekiya, nati, Tayeretsa nyumba yonse ya Yehova, ndi guwa la nsembe yopsereza, ndi zipangizo zace zonse, ndi gome la mkate woonekera, ndi zipangizo zace zonse.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 29

Onani 2 Mbiri 29:18 nkhani