Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 29:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ananyamuka Alevi, Mahati mwana wa Amasai ndi Yoeli mwana wa Azariya, a ana a Akohati; ndi a ana a Merari, Kisi mwana wa Abidi, ndi Azariya mwana wa Yehaleleli; ndi a Agerisoni, Yowa mwana wa Zima, ndi Edeni mwana wa Yowa;

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 29

Onani 2 Mbiri 29:12 nkhani