Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 28:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Yehova Mulungu wace anampereka m'dzanja la mfumu ya Aramu; ndipo anamkantha, natenga ndende unyinji waukuru wa anthu ace, nafika nao ku Damasiko. Anaperekedwanso iye m'dzanja la mfumu ya Israyeli, amene anamkantha makanthidwe akuru.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 28

Onani 2 Mbiri 28:5 nkhani