Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 26:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu Uziya anali wakhate mpaka tsiku la imfa yace, nakhala m'nyumba ya padera, popeza ndiye wakhate; pakuti anadulidwa ku nyumba ya Yehova; ndi Yotamu mwana wace anayang'anira nyumba ya mfumu naweruza anthu a m'dziko.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 26

Onani 2 Mbiri 26:21 nkhani