Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 26:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma atakhala wamphamvu, mtima wace unakwezeka momuononga, nalakwira Yehova Mulungu wace; popeza analowa m'Kacisi wa Yehova kufukiza pa guwa la nsembe la cofukiza.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 26

Onani 2 Mbiri 26:16 nkhani