Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 26:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Namanga nsanja m'cipululu, nakumba zitsime zambiri; popeza anali nazo zoweta zambiri; kumadambo, ndi kuzidikha; nakhala nao olima minda, ndi osunga mpesa kumapiri ndi ku nthaka yopatsa bwino; pakuti ndiye mlimi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 26

Onani 2 Mbiri 26:10 nkhani