Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 25:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cipambukire Amaziya kusatsata Yehova, anamcitira ciwembu m'Yerusalemu, nathawira ku Lakisi iyeyu; koma anatuma omtsatira ku Lakisi, namupha komweko.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25

Onani 2 Mbiri 25:27 nkhani