Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 25:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoasi mfumu ya Israyeli anagwira Amaziya mfumu ya Yuda, mwana wa Yoasi mwana wa Yehoahazi, ku Betisemesi, nabwera naye ku Yerusalemu, nagamula linga la Yerusalemu kuyambira cipata ca Efraimu kufikira cipata ca kungondya, mikono mazana anai.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25

Onani 2 Mbiri 25:23 nkhani