Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 24:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Omcitira ciwembu ndi awa: Zabadi, mwana wa Simeati wamkazi M-amoni; ndi Yozabadi, mwana wa Simiriti wamkazi Mmoabu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 24

Onani 2 Mbiri 24:26 nkhani