Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 23:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Natenga atsogoleri a mazana, ndi omveka, ndi akazembe a anthu, ndi anthu onse a m'dziko, natsika ndi mfumu ku nyumba ya Yehova; nalowera pa cipata ca kumtunda m'nyumba ya mfumu, namkhalitsa mfumu pa mpando wa ufumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 23

Onani 2 Mbiri 23:20 nkhani