Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 23:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehoyada anaika mayang'aniro a nyumba ya Yehova m'dzanja la ansembe Aleviwo, amene Davide anawagawa, ayang'anire nyumba ya Yehova; napereka nsembe zopsereza za Yehova monga mulembedwa m'cilamulo ca Mose, ndi kukondwera ndi kuyimbira, monga mwa cilangizo ca Davide.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 23

Onani 2 Mbiri 23:18 nkhani