Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 23:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehoyada wansembe anaturuka nao atsogoleri a mazana akuyang'anira khamu la nkhondo, nanena nao, Mturutseni mkaziyo pakati pa mipambo; ndipo ali yense womtsata aphedwe ndi lupanga; pakuti wansembe adati, Msamphere m'nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 23

Onani 2 Mbiri 23:14 nkhani