Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 21:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cinkana anatero, Aedomu anapanduka kupulumuka m'dzanja la Yuda mpaka lero lino; nthawi yomweyo anapanduka Alibina kupulumuka m'dzanja lace; cifukwa adasiya Yehova Mulungu wa makolo ace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 21

Onani 2 Mbiri 21:10 nkhani