Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 20:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anabwerera amuna onse a Yuda, ndi a ku Yerusalemu, nawatsogolera ndi Yehosafati, kubwerera kumka ku Yerusalemu ndi cimwemwe; pakuti Yehova anawakondweretsa pa adani ao.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 20

Onani 2 Mbiri 20:27 nkhani