Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 20:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehosafati anawerama mutu wace, nkhope yace pansi; ndi Ayuda onse, ndi okhala m'Yerusalemu anagwa pansi pamaso pa Yehova, nalambira Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 20

Onani 2 Mbiri 20:18 nkhani