Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 2:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsono munditumizire munthu wa luso lakucita ndi golidi, ndi siliva, ndi mkuwa, ndi citsulo, ndi thonje lofiirira, ndi lofiira, ndi lamadzi, wakudziwa kuzokota zozokota ziri zonse, akhale ndi amuna aluso okhala ndi ine m'Yuda ndi m'Yerusalemu, amene Davide atate wanga anawakonzeratu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 2

Onani 2 Mbiri 2:7 nkhani