Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 2:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo anawerenga alendo Onse okhala m'dziko la Israyeli, monga mwa mawerengedwe aja atate wace Davide adawawerenga nao, nawapeza afikira zikwi zana limodzi mphambu makumi asanu kudza zitatu ndi mazana asanu ndi limodzi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 2

Onani 2 Mbiri 2:17 nkhani