Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 2:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, ndidzawapatsa anyamata anu otema akulikha mitengo miyeso ya tirigu wopuntha zikwi makumi awiri, ndi miyeso ya barele zikwi makumi awiri, ndi mitsuko yaikuru ya vinyo zikwi makumi awiri, ndi mitsuko yaikufu ya mafuta zikwi makumi awiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 2

Onani 2 Mbiri 2:10 nkhani