Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 19:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ukakudzerani mlandu uli wonse wocokera kwa abale anu okhala m'midzi mwao, kusiyanitsa pakati pa mwazi ndi mwazi, pakati pa cilamulo ndi ciuzo, malemba ndi maweruzo, muwacenjeze kuti asaparamule kwa Yehova, angafikitsire inu nokha ndi abale anu mkwiyo; muzitero, ndipo simudzaparamula.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 19

Onani 2 Mbiri 19:10 nkhani