Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 18:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Ndinaona Aisrayeli onse obalalika pamapiri ngati nkhosa zopanda mbusa; nati Yehova, Awa alibe mbuye wao, abwerere yense ku nyumba yace mumtendere.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 18

Onani 2 Mbiri 18:16 nkhani