Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 18:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene anafika kwa mfumu, mfumu inanena naye, Mikaya timuke ku Ramoti Gileadi kunkhondo kodi, kapena ndileke? Nati iye, Kwerani, mudzacita mwai; ndipo adzaperekedwa m'dzanja lanu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 18

Onani 2 Mbiri 18:14 nkhani