Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 17:17-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. ndi a Benjamini: Eliyada ngwazi yamphamvu, ndi pamodzi ndi iye zikwi mazana awiri ogwira mauta ndi zikopa;

18. wotsatana naye Yozabadi, ndi pamodzi ndi iye okonzekeratu ku nkhondo zikwi zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu.

19. Ndiwo amene analindirira mfumu, osawerenga iwo aja mfumu adawaika m'midzi yamalinga m'Yuda monse.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 17