Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 17:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Afilisti ena anabweca nazo kwa Yehosafati mitulo, ndi ndalama za msonkho; Aarabu omwe anabwera nazo kwa iye zoweta, nkhosa zamphongo zikwi zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu ndi awiri ndi atonde zikwi zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 17

Onani 2 Mbiri 17:11 nkhani