Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 15:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Namemezaonse a m'Yuda ndi m'Benjamini, ndi iwo akukhala nao ocokera ku Efraimu, ndi Manase, ndi Simeoni; pakuti anamdzera ocuruka ocokera ku Israyeli, pamene anaona kuti Yehova Mulungu wace anali naye.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 15

Onani 2 Mbiri 15:9 nkhani