Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 15:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo anaturuka kukomana naye Asa, nanena naye, Mundimvere, Asa, ndi onse Ayuda ndi Abenjamini, Yehova ali nanu; mukakhala ndi Iye, mukamfuna Iye, mudzampeza; koma mukamsiya, adzakusiyani.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 15

Onani 2 Mbiri 15:2 nkhani