Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 14:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Asa anapfuulira kwa Yehova Mulungu wace, nati, Yehova, palibe wina ngati Inu, kuthandiza pakati pa wamphamvu ndi iye wopanda mphamvu; tithandizeni Yehova Mulungu wathu, titama Inu, taturukira aunyinji awa m'dzina lanu. Yehova, Inu ndinu Mulungu wathu, munthu asakulakeni.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 14

Onani 2 Mbiri 14:11 nkhani