Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 12:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sisaki mfumu ya Aigupto anakwerera Yerusalemu, nacotsa cuma ca m'nyumba ya Yehova, ndi cuma ca m'nyumba ya mfumu; anazicotsa zonse; anacotsanso zikopa zagolidi adazipanga Solomo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 12

Onani 2 Mbiri 12:9 nkhani