Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 12:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Macitidwe ace tsono a Rehabiamu, zoyamba ndi zotsiriza, sizilembedwa kodi m'buku la mau a Semaya mneneriyo, ndi la Ido mlauliyo, lakunena za zibadwidwe? Ndipo panali nkhondo pakati pa Rehabiamu ndi Yerobiamu masiku onse.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 12

Onani 2 Mbiri 12:15 nkhani