Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 9:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nalowa, ndipo taonani, akazembe a khamu alikukhala pansi; nati iye, Ndiri ndi mau kwa inu, kazembe. Nati Yehu, Kwa yani wa ife tonse? Nati iye, Kwa Inu, kazembe.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:5 nkhani