Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 9:36-37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

36. Nabwerera iwo, namfotokozera. Nati iye, Ndiwo mau a Yehova ananena wo mwa mtumiki wace Eliya wa ku Tisibe, ndi koti, Pa munda wa Yezreeli agaru adzadya mnofu wa Yezebeli;

37. ndi thupi la Yezebeli lidzakhala ngati ndowe pamunda m'dera la Yezreeli, kuti sadzati, Ndi Yezebeli uyu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9