Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 9:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pofika Yehu ku Yezreeli, Yezebeli anamva, nadzikometsera m'maso, naluka tsitsi lace, nasuzumira pazenera.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:30 nkhani