Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 9:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Yehu kwa Bidikara kazembe wace, Mnyamule, numponye m'munda wa Naboti wa ku Yezreeli; pakuti kumbukila m'mene ine ndi iwe tinali pa akavalo athu pamodzi kutsata Ahabu atate wace, Yehova anamsenzetsa katundu uyu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:25 nkhani