Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 9:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nafulumira iwo, nagwira yense copfunda cace, naciyala pokhala iye paciunda, naomba lipenga, nati, Yehu ndiye mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:13 nkhani