Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 9:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Elisa mneneriyo anaitana mmodzi wa ana a aneneri, nanena naye, Udzimangire m'cuuno, nutenge nsupa iyi ya mafuta m'dzanja mwako, numuke ku Ramoti Gileadi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:1 nkhani