Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 8:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, alimkufotokozera mfumu m'mene adamuukitsira wakufayo, taonani, mkaziyo adamuukitisira mwana wace ananena za nyumba yace ndi munda wace kwa mfumu. Nati Gehazi, Mbuye wanga mfumu, suyu mkaziyo, suyu mwana wace Elisa anamuukitsayo?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:5 nkhani