Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 7:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza Yehova adamvetsa khamu la Aaramu phokoso la magareta ndi mkokomo wa akavalo, phokoso la nkhondo yaikuru; nanenana wina ndi mnzace, Taonani mfumu ya Israyeli watimemezera mafumu a Ahiti ndi mafumu a Aaigupto, atigwere.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:6 nkhani